2 Akorinto 13:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo tipemphera Mulungu kuti musacite kanthu koipa; sikuti ife tikaoneke obvomerezeka, koma kuti inu mukacite cabwino, tingakhale ife tikhala monga osatsimikizidwa.

2 Akorinto 13

2 Akorinto 13:1-8