2 Akorinto 13:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

pakuti anapacikidwa m'ufoko, koma ali ndi moyo mu mphamvu ya Mulungu. Pakuti ifenso tiri ofok a mwa iye, koma tidzakhala ndi moyo pamodzi ndi iye, mu mphamvu ya Mulungu, ya kwa inu.

2 Akorinto 13

2 Akorinto 13:1-11