2 Akorinto 13:13-14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

13. Oyera mtima onse alankhula inu,

14. Cisomo ca Ambuye Yesu Kristu, ndi cikondi ca Mulungu, ndi ciyanjano ca Mzimu Woyera zikhale ndi inu nonse.

2 Akorinto 13