2 Akorinto 12:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndidziwa munthu wa mwa Kristu, zitapita zaka khumi ndi zinai (ngati m'thupi, sindidziwa; ngati kunja kwa thupi, sindidziwa; adziwa Mulungu), anakwatulidwa wotereyo kunka naye Kumwamba kwacitatu.

2 Akorinto 12

2 Akorinto 12:1-10