2 Akorinto 12:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Taonani, nthawi yaitatu iyi ndapukwa ine kudza kwa nu, ndipo sindidzakusaukitsani; pakuti sindifuna zanu, koma inu; cakuti ana sayenera kuunjikira atate adi amai, koma atate ndi amai kumjikira ana.

2 Akorinto 12

2 Akorinto 12:5-21