2 Akorinto 12:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace ndisangalala m'tnaufoko, m'ziwawa, m'zikakamizo, m'mazunzo, m'zipsinjiko, cifukwa ca Kristu; pakuti pamene ndifoka, pamenepo ndiri wamphamvu.

2 Akorinto 12

2 Akorinto 12:5-12