2 Akorinto 11:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakutitu ngati iye wakudza alalikira Yesu wina, amene ife sitinalalikira, kapena ngati mulandira mzimu wa mtundu wina, umene simunalandira, kapena uthenga wabwino wa mtundu wina umene simunalandira, mulolana nave bwino lomwe.

2 Akorinto 11

2 Akorinto 11:1-5