2 Akorinto 10:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

osadzitamandira popitirira muyeso mwa macititso a ena; koma tiri naco ciyembekezo kuti pakukula cikhulupiriro canu, tidzakulitsidwa mwa inu monga mwa cilekezero cathu kwa kucurukira,

2 Akorinto 10

2 Akorinto 10:9-18