1 Yohane 4:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Munthu akati, kuti, Ndikonda Mulungu, nadana naye mbale wace, ali wabodza: pakuti iye wosakonda mbale ware amene wamuona, sakhoza kukonda Mulungu amene sanamuona.

1 Yohane 4

1 Yohane 4:15-21