1 Yohane 4:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Palibe munthu adamuona Mulungu nthawi iri yonse; tikakondana wina ndi mnzace, Mulungu akhala mwa ife, ndi cikondi cace cikhala cangwiro mwa ife;

1 Yohane 4

1 Yohane 4:6-13