1 Yohane 3:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

iye wocita cimo ali wocokera mwa mdierekezi, cifukwa mdierekezi amacimwa kuyambira paciyambi. Kukacita ici Mwana wa Mulungu adaonekera, ndiko kuti akaononge nchito za mdierekezi,

1 Yohane 3

1 Yohane 3:2-11