1 Yohane 2:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndikulemberani, atate, popeza mwamzindikira iye amene ali kuyambir paciyambi. Ndikulemberani anyamata, popeza mwamlaka woipavo, Ndakulemberani, ana, popeza mwazindikira Atate.

1 Yohane 2

1 Yohane 2:3-22