1 Yohane 1:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

cimene tidaciona, ndipo tidacimva, tikulatikirani inunso, kuti inunso mukayaniane pamodzi ndi ife; ndipo ciyanjano cathu cirinso ndi Atate, ndipo ndi Mwana wace Yesu Kristu;

1 Yohane 1

1 Yohane 1:1-10