1 Timoteo 5:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma ngati wamasiye wina ali nao ana kapena adzukulu, ayambe aphunzire iwo kucitira ulemu a m'banja lao, ndi kubwezera akuwabala; pakuti ici ncolandirika pamaso pa Mulungu.

1 Timoteo 5

1 Timoteo 5:1-13