1 Timoteo 5:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Mkulu usamdzudzule, komatu umdandaulire ngati atate; anyamata ngati abale;

2. akazi akulu ngati amai; akazi ang'ono ngati alongo, m'kuyera mtima konse.

1 Timoteo 5