1 Timoteo 4:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti kukalingako tlgwiritsa nchito ndi kuyesetsa, cifukwa ciyembekezo cathu tiri naco pa Mulungu wamoyo, amene ali Mpulumutsi wa anthu onse, makamaka wa okhulupira.

1 Timoteo 4

1 Timoteo 4:7-16