1 Timoteo 1:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

podziwa ici, kuti lamulo siliikika kwa munthu wolungama, koma kwa osayeruzika ndi osamvera lamulo, osapembedza, ndi ocimwa, osalemekeza ndi amnyozo, akupha atate ndi akupha amai, akupha anzao,

1 Timoteo 1

1 Timoteo 1:2-10