1 Timoteo 1:19-20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

19. ndi kukhala naco cikhulupiriro ndi cikumbu mtima cokoma, cimene ena adacikankha, cikhulupiriro cao cidatayika;

20. a iwo ali Humenayo ndi Alesandro, amene ndawapereka kwa Satana, kuti aphunzire kusalankhula zamwano.

1 Timoteo 1