1 Timoteo 1:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndingakhale kale ndinali wamwano, ndi wolondalonda, ndi wacipongwe; komatu anandicitira cifundo, popeza ndinazicita wosazindikira, wosakhulupirira;

1 Timoteo 1

1 Timoteo 1:5-16