1 Samueli 9:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma ananena naye, Onatu, m'mudzi muno muli munthu wa Mulungu, ndiye munthu anthu amcitira ulemu; zonse azinena zicitika ndithu; tiyeni tipite komweko, kapena adzakhoza kutidziwitsa zimene tirikuyendera.

1 Samueli 9

1 Samueli 9:1-12