1 Samueli 9:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo aburu a Kisi, atate wa Sauli, analowerera. Ndipo Kisi anati kwa Sauli mwana wace, Utenge mnyamata mmodzi, nunyamuke, kukafuna aburuwo.

1 Samueli 9

1 Samueli 9:1-13