1 Samueli 9:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Samueli anatenga Sauli ndi mnyamata wace, napita nao ku cipinda ca alendo, nawakhalitsa pa malo a ulemu pakati pa oitanidwa onse; ndiwo anthu monga makumi atatu.

1 Samueli 9

1 Samueli 9:18-27