1 Samueli 9:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Samueli anayankha Sauli nati, Inendinemlauliyo. Kwera, batsogola kumsanje, pakuti mudzadya ndi ine lero; ndipo m'mawa ndidzakulola upite, ndi kukudziwitsa zonse ziri mumtima mwako.

1 Samueli 9

1 Samueli 9:15-27