1 Samueli 8:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipotsiku lija mudzapfuula cifukwa ca mfumu yanu munadzisankhira nokha; koma Yehova sadzayankha inu tsiku lijalo.

1 Samueli 8

1 Samueli 8:11-22