1 Samueli 7:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ana a Israyeli anati kwa Samueli, Musaleke kutipempherera kwa Yehova Mulungu wathu, kuti iye atipulumutse m'manja a Afilistiwo.

1 Samueli 7

1 Samueli 7:4-12