1 Samueli 7:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anaunjikana ku Mizipa, natunga madzi, nawatsanula pamaso pa Yehova, nasala cakudya tsiku lija, nati, Tinacimwira Yehova. Ndipo Samueli anaweruza ana a Israyeli m'Mizipa.

1 Samueli 7

1 Samueli 7:2-14