1 Samueli 7:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali, kuti likasalo linakhala nthawi yaikuru m'Kiriati-yearimu; popeza linakhalako zaka makumi awiri; ndipo banja lonse la Israyeli linalirira Yehova.

1 Samueli 7

1 Samueli 7:1-6