1 Samueli 7:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anabwera ku Rama, pakuti nyumba yace inali kumeneko; ndipo pamenepo anaweruza Israyeli; namangapo guwa la nsembe la Yehova.

1 Samueli 7

1 Samueli 7:10-17