1 Samueli 6:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo garetalo linafika m'munda wa Yoswa wa ku Betisemesi, ndi kuima momwemo, pa mwala waukuru; ndipo anawaza matabwa a garetalo, nazipereka ng'ombezo nsembe yopsereza kwa Yehova.

1 Samueli 6

1 Samueli 6:6-16