1 Samueli 5:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Yehova anabvuta iwo a ku Asidodi ndi dzanja lace, nawaononga, nawazunza ndi mafundo, m'Asidodi ndi m'miraga yace.

1 Samueli 5

1 Samueli 5:2-12