1 Samueli 4:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo munthu wa pfuko la Benjamini anathamanga kucokera ku khamu la ankhondo, nafika ku Silo tsiku lomwelo, ndi zobvala zace zong'ambika, ndi dothi pamutu pace.

1 Samueli 4

1 Samueli 4:7-13