1 Samueli 4:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mau a Samueli anafikira kwa Aisrayeli onse. Ndipo Aisrayeli anaturuka kukaponyana nkhondo ndi Afilisti, namanga zithando zao ku Ebenezeri; Afilistiwo namanga m'Afeki.

1 Samueli 4

1 Samueli 4:1-5