1 Samueli 31:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pakuona kuti Sauli anafa, wonyamula zida zace yemwe, anagwera lupanga lace, nafera limodzi ndi iye.

1 Samueli 31

1 Samueli 31:1-10