1 Samueli 30:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Davide anadololoka kwambiri, pakuti anthu ananena za kumponya iye miyala, pakuti mtima wao wa anthu onse unali ndi cisoni, yense cifukwa ca ana ace amuna ndi akazi. Koma Davide anadzilimbikitsa mwa Yehova Mulungu wace.

1 Samueli 30

1 Samueli 30:1-15