1 Samueli 30:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo anthu oipa onse, ndi opanda pace a iwo amene anapita ndi Davide anayankha nati, Popeza sadamuka nafe sitidzawapatsa kanthu ka zofunkha tidazilanditsa, koma kwa munthu yense mkazi wace ndi ana ace, kuti acoke nao namuke.

1 Samueli 30

1 Samueli 30:14-31