1 Samueli 30:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Davide anawalondola, iye ndi anthu mazana anai; koma anthu mazana awiri anatsala m'mbuyo, cifukwa analema, osakhoza kuoloka kamtsinje Besori.

1 Samueli 30

1 Samueli 30:1-11