1 Samueli 28:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Davide anati kwa Akisi, Potero mudzadziwe cimene mnyamata wanu adzacita. Ndipo Akisi anati kwa Davide, Cifukwa cace ndidzakuika iwe ukhale wondisungira moyo wanga masiku onse.

1 Samueli 28

1 Samueli 28:1-9