1 Samueli 28:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova yekha wacita monga ananena pakamwa panga; ndipo Yehova wang'amba ufumuwo, kuucotsa m'dzanja lako, ndi kuupatsa mnansi wako, ndiye Davide.

1 Samueli 28

1 Samueli 28:10-18