1 Samueli 28:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ananena naye, Makhalidwe ace ndi otani? nati iye, Nkhalamba irikukwera yobvala mwinjiro. Pamenepo Sauli anazindikira kuti ndi Samueli, naweramitsa nkhope yace pansi, namgwadira.

1 Samueli 28

1 Samueli 28:12-21