1 Samueli 27:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Davide anapasula dzikolo, sanasunga ndi moyo mwamuna kapena wamkazi; natenga nkhosa, ndi ng'ombe, ndi aburu, ndi ngamila, ndi zobvala; nabwera nafika kwa Akisi.

1 Samueli 27

1 Samueli 27:2-12