1 Samueli 27:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Akisi anampatsa Zikilaga tsiku lomweli; cifukwa cace Zikilaga ndi wa mafumu a Yuda kufikira lero lomwe.

1 Samueli 27

1 Samueli 27:5-12