1 Samueli 27:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Davide ananyamuka, naoloka pamodzi ndi anthu mazana asanu ndi limodzi amene anali naye, nafika kwa Akisi mwana wa Maoki, mfumu ya ku Gati.

1 Samueli 27

1 Samueli 27:1-6