1 Samueli 27:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Davide sadasunga wamoyo mwamuna kapena mkazi, kubwera nao ku Gati; popeza adati, Kuti angatiulule, ndi kuti, Davide anatero, ndi makhalidwe ace ndi otere, masiku onse akukhala ku dziko la Afilisti.

1 Samueli 27

1 Samueli 27:2-12