1 Samueli 26:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova adzabwezera munthu yense cilungamo cace ndi cikhulupiriko cace, popeza Yehova anakuperekani lero m'dzanja langa, koma sindinalola kutukulira dzanja langa pa wodzozedwa wa Yehova,

1 Samueli 26

1 Samueli 26:15-25