1 Samueli 25:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Davide natuma anyamata khumi, nanena kwa anyamatawo, Mukwere ku Karimeli, mumuke kwa Nabala ndi kundilankhulira iye;

1 Samueli 25

1 Samueli 25:4-8