1 Samueli 25:44 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti Sauli anapatsa Mikala, mwana wace, mkazi wa Davide, kwa Paliti mwana wa Loisi, wa ku Galimu.

1 Samueli 25

1 Samueli 25:34-44