1 Samueli 25:42 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Abigayeli anafulumira nanyamuka, nakwera pa bum, pamodzi ndi anamwali ace asanu akumtsata; natsatira mithenga ya Davide, nakhala mkazi wace.

1 Samueli 25

1 Samueli 25:35-44