1 Samueli 25:34 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti ndithu, Pali Yehova Mulungu wa Israyeli, amene anandiletsa lero kusapweteka iwe, ukadapanda kufulumira kubwera kundicingamira, zoonadi sindikadasiyira Nabala kufikira kutaca kanthu konse, ngakhale mwana wamwamunammodzi.

1 Samueli 25

1 Samueli 25:30-35