1 Samueli 25:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mukhululukire kulakwa kwa mdzakazi wanu; pakuti Yehova adzapatsadi mbuye wanga banja lokhazikika, pakuti mbuyanga amaponya nkhondo za Yehova; ndipo mwa inu simudzapezeka coipa masiku anu onse.

1 Samueli 25

1 Samueli 25:19-35