1 Samueli 25:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma mnyamata wina anauza Abigayeli, mkazi wa Nabala, kuti, Onani, Davide anatumiza mithenga akucokera kucipululu kulankhula mbuye wathu; koma iye anawakalipira.

1 Samueli 25

1 Samueli 25:4-17